1 Chronicles 16:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tamandani Chauta, inu anthu a mitundu yonse, vomerezani kuti ulemerero ndi mphamvu, zonse nza Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mchitireni Yehova, inu mafuko a mitundu ya anthu, mchitireni Yehova ulemerero ndi mphamvu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Perekani kwa Yehova, Inu mabanja a anthu a mitundu ina, perekani kwa Yehova ulemerero ndi mphamvu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mcitireni Yehova, inu mafuko a mitundu ya anthu, Mcitireni Yehova ulemerero ndi mphamvu.