1 Chronicles 16:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Njenjemerani pamaso pake, inu anthu onse a pa dziko lapansi. Ndithu dziko lapansi lakhazikika kolimba, osatha kuligwedeza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Njenjemerani pamaso pake, inu dziko lonse lapansi, dziko lokhalamo anthu lomwe lakhazikika, kuti silingagwedezeke.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Njenjemerani pamaso pake, dziko lonse lapansi! Dziko linakhazikika kolimba; silingasunthidwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Njenjemerani pamaso pace, inu dziko lonse lapansi, Dziko lokhalamo anthu lomwe lakhazikika, kuti silingagwedezeke.