1 Chronicles 16:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zakumwamba zisangalale, za pansi pano zikondwere, zonsezo zilengeze kwa anthu onse kuti, “Chauta ndiye mfumu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kukondwerere kumwamba, ndi dziko lapansi lisekerere; anene mwa amitundu, Yehova achita ufumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zakumwamba zisangalale, dziko lapansi likondwere; anene anthu a mitundu ina, “Yehova ndi mfumu!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kukondwerere kumwamba, ndi dziko lapansi lisekerere; Anene mwa amitundu, Yehova acita ufumu.