1 Chronicles 16:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mitengo yam'nkhalango idzaimbira Chauta mokondwa, pamene adzabwera kudzalamulira dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo mitengo yonse ya kunkhalango idzafuula mokondwera pamaso pa Yehova; pakuti akudza kudzaweruza dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo mitengo ya mʼnkhalango idzayimba, idzayimba chifukwa cha chimwemwe pamaso pa Yehova, pakuti akubwera kudzaweruza dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo mitengo yonse ya kunkhalango idzapfuula mokondwera pamaso pa Yehova; Pakuti akudza kudzaweruza dziko lapansi,