1 Chronicles 16:37 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Davide adasiya Asafu pamodzi ndi abale ake kumene kunali Bokosi lachipangano la Chauta, kuti azitumikira nthaŵi zonse ku Bokosilo monga m'mene kunkafunikira tsiku lililonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anasiyako ku likasa la chipangano la Yehova Asafu ndi abale ake, atumikire kulikasa kosalekeza, monga umo mudzafunika tsiku ndi tsiku;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Davide anasiya Asafu pamodzi ndi anzake kumene kunali Bokosi la Chipangano la Yehova kuti azitumikira kumeneko nthawi zonse, monga mwa zoyenera kuchita pa tsiku lililonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anasiyako ku likasa la cipangano la Yehova Asafu ndi abale ace, atumikire kulikasa kosalekeza, monga umo mudzafunika tsiku ndi tsiku;