1 Chronicles 16:38 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Obededomu pamodzi ndi abale ake 68 ankathandizana nawo pa ntchitoyo. Nthaŵi imeneyo Obededomu, mwana wa Yedutuni, ndiponso Hosa, anali ndi udindo wolonda pa makomo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Obededomu, ndi abale ake makumi asanu ndi limodzi mphambu asanu ndi atatu; ndi Obededomu mwana wa Yedutuni ndi Hosa akhale odikira;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anasiyanso Obedi-Edomu pamodzi ndi anzake 68 kuti azitumikira nawo pamodzi. Obedi-Edomu mwana wa Yedutuni ndi Hosa anali alonda a pa chipata.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Obedi Edomu, ndi abale ace makumi asanu ndi limodzi mphambu asanu ndi atatu; ndi Obedi Edomu mwana wa Yedutuni ndi Hosa akhale odikira;