1 Chronicles 16:40 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaŵasiya kumeneko kuti azipereka nthaŵi zonse nsembe zopsereza kwa Chauta pa guwa la nsembe zopsereza, m'maŵa ndi madzulo, potsata zonse zimene zidalembedwa m'buku la Malamulo a Mose amene Chauta adalamula Aisraele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kupereka nsembe zopsereza kwa Yehova pa guwa la nsembe zopsereza, kosalekeza, m'mawa ndi madzulo, monga mwa zonse zilembedwa m'chilamulo cha Yehova adachilamulira Israele;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti azipereka nsembe zopsereza kwa Yehova pa guwa lansembe nthawi zonse mmawa ndi madzulo, potsata zonse zimene zinalembedwa mʼbuku la malamulo a Yehova, amene anawapereka kwa Aisraeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kupereka nsembe zopsereza kwa Yehova pa guwa la nsembe zopsereza, kosalekeza, m'mawa ndi madzulo, monga mwa zonse zilembedwa m'cilamulo ca Yehova adacilamulira Israyeli;