1 Chronicles 16:43 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake anthu onse adachoka, aliyense kupita kunyumba kwake. Davide nayenso adapita kwao kuti akadalitse banja lake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anachoka anthu onse, yense kunyumba yake, nabwera Davide kudalitsa nyumba yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anthu onse anachoka, aliyense kupita kwawo. Ndipo Davide anabwerera ku nyumba kwake kukadalitsa banja lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anacoka anthu onse, yense ku nyumba yace, nabwera Davide kudalitsa nyumba yace.