1 Chronicles 17:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuyambira nthaŵi imene ndidaaika aweruzi a anthu anga Aisraele. Choncho ndidagonjetsa adani ako onse. Kuonjezera pamenepo, ndikukuuza kuti Ine Chauta ndidzakhazikitsa banja lako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kuyambira kuja ndinaika oweruza ayang'anire anthu anga Israele; ndipo ndagonjetsa adani ako onse. Ndikuuzanso kuti Yehova adzakumangira banja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
monga akhala akuchitira kuchokera nthawi imene ndinasankha atsogoleri a anthu anga Aisraeli. Ine ndidzagonjetsanso adani anu onse. “ ‘Ine ndikulengeza kwa iwe kuti Yehova adzakhazikitsa banja lako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kuyambira kuja ndinaika oweruza ayang'anire anthu anga Israyeli; ndipo ndagonjetsa adani ako onse. Ndikuuzanso kuti Yehova adzakumangira banja.