1 Chronicles 17:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ndidzamkhalitsa mu Nyumba yanga ndi mu ufumu wanga, ndipo ufumu wake udzakhala mpaka muyaya.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma ndidzamkhazikitsa m'nyumba mwanga, ndi m'ufumu wanga kosatha; ndi mpando wa chifumu wake udzakhazikika kosatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzamuyika kukhala wolamulira nyumba yanga ndi ufumu wanga kwamuyaya. Mpando wake waufumu udzakhazikika kwamuyaya.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma ndidzamkhazikitsa m'nyumba mwanga, ndi m'ufumu wanga kosatha; ndi mpando wa cifumu wace udzakhazikika kosatha.