1 Chronicles 17:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo nchiyaninso chimene Davide anganene kwa Inu, popeza kuti mwamchitira ulemu chotere mtumiki wanu? Zoonadi Inu mumamdziŵa mtumiki wanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anenenjinso Davide kwa inu za ulemu wochitikira mtumiki wanu? Pakuti mudziwa mtumiki wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kodi Davide anenenso chiyani kwa Inu, pakuti mwachitira ulemu wotere mtumiki wanu? Pakuti Inu mukumudziwa mtumiki wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anenenjinso Davide kwa Inu za ulemu wocitikira mtumiki wanu? pakuti mudziwa mtumiki wanu.