1 Chronicles 17:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa chokonda mtumiki wanu, ndiponso malinga ndi mtima wanu, Inu Chauta, mwachita chinthu chachikulu choterechi, pondidziŵitsa zakutsogolozi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova, chifukwa cha mtumiki wanu, ndi monga mwa mtima wanu, mwachita ukulu uwu wonse, kundidziwitsa zazikulu izi zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu Yehova, chifukwa cha mtumiki wanu komanso mwa chifuniro chanu, mwachita chinthu chachikulu ichi ndipo mwawulula malonjezo anu aakulu onse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova, cifukwa ca mtumiki wanu, ndi monga mwa mtima wanu, mwacita ukulu uwu wonse, kundidziwitsa zazikuru izi zonse.