1 Chronicles 17:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Natani adauza Davide kuti, “Ai, chitani chilichonse chimene mukuganiza mumtima mwanu, poti Mulungu ali nanu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Natani anati kwa Davide, Muchite zonse zili m'mtima mwanu; pakuti Mulungu ali nanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Natani anayankha Davide kuti, “Chitani chilichonse chimene chili mu mtima mwanu, chifukwa Mulungu ali nanu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Natani anati kwa Davide, Mucite zonse ziri m'mtima mwanu; pakuti Mulungu ali nanu.