1 Chronicles 17:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mudaŵasandutsa anthu anu Aisraele kuti akhale anthu anu mpaka muyaya, ndipo Inu Chauta mudakhala Mulungu wao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti anthu anu Israele mudawayesa anthu anuanu kosatha; ndipo Inu, Yehova, munayamba kukhala Mulungu wao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu munawapanga anthu anu Aisraeli kukhala anuanu kwamuyaya, ndipo Inu, Inu Yehova ndinu Mulungu wawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti anthu anu Israyeli mudawayesa anthu anu anu kosatha; ndipo Inu, Yehova, munayamba kukhala Mulungu wao.