1 Chronicles 18:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa nthaŵi imeneyi Abisai, mwana wa Zeruya, adapha Aedomu okwanira 18,000 ku chigwa cha Mchere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Abisai mwana wa Zeruya anakantha Aedomu m'Chigwa cha Mchere zikwi khumi mphambu zisanu ndi zitatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abisai mwana wa Zeruya anakantha Aedomu 18,000 mu Chigwa cha Mchere.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Abisai mwana wa Zeruya anakantha Aedomu m'Cigwa ca Mcere zikwi khumi mphambu zisanu ndi zitatu.