1 Chronicles 18:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Davide adaika ankhondo pena ndi pena m'dziko la Edomu, ndipo Aedomu onse adasanduka anthu otumikira Davideyo. Motero Chauta adampambanitsa Davide kulikonse kumene ankapita.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anaika asilikali a boma m'Edomu; ndi Aedomu onse anasanduka anthu a Davide. Ndipo Yehova anasunga Davide kulikonse anamukako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anayika maboma ku Edomu, ndipo Aedomu onse anakhala pansi pa Davide. Yehova ankapambanitsa Davide kulikonse kumene ankapita.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaika asilikari a boma m'Edomu; ndi Aedomu onse anasanduka anthu a Davide. Ndipo Yehova anasunga Davide kuli konse anamukako.