1 Chronicles 19:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ena onse otsala adaŵaika m'manja mwa Abisai, mbale wake, ndipo adaŵandanditsa moyang'anana ndi Aamoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu otsala anawapereka m'dzanja la Abisai mbale wake; ndipo anadzinika ayambane ndi ana a Amoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anayika ankhondo ena otsalawo mʼmanja mwa Abisai mʼbale wake ndipo anawayika kuti amenyane ndi Aamoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu otsala anawapereka m'dzanja la Abisai mbale wace; ndipo anadzinika avambane ndi ana a Amoni.