1 Chronicles 19:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Yowabu adauza Abisai kuti, “Ngati Asiriya andipose mphamvu, iwe udzandithandize. Koma ngati Aamoni akupose mphamvu, ineyo ndidzabwera kudzakuthandiza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati, Akandiposa mphamvu Aaramu, udzandilanditsa ndiwe; koma akakuposa mphamvu ana a Amoni, ndidzakulanditsa ndine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yowabu anati, “Ngati Aaramu andipose mphamvu, iwe ubwere udzandipulumutse; koma ngati Aamoni akupose mphamvu, ine ndidzabwera kudzakupulumutsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati, Akandilaka Aaramu, udzandilanditsa ndiwe; koma akakulaka ana a Amoni, ndidzakulanditsa ndine.