1 Chronicles 19:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho Yowabu ndi anthu ake adasendera pafupi ndi Asiriyawo kuti amenyane nawo nkhondo, koma Asiriyawo adathaŵa iye akufika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Yowabu ndi anthu anali naye anayandikira pamaso pa Aaramu kulimbana nao, ndipo anawathawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Yowabu ndi ankhondo amene anali naye anapita kukamenyana ndi Aaramu, ndipo iwo anathawa pamaso pake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Yoabu ndi anthu anali naye anayandikira pamaso pa Aaramu kulimbana nao, ndipo anawathawa.