1 Chronicles 19:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho Hanuni adagwira atumiki a Davide aja naŵameta ndevu mwachiperengedzu. Kenaka adadula zovala zao pakati mpaka m'chiwuno, naŵabweza kwao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Hanuni anatenga anyamata a Davide, nawameta, nadula malaya ao pakati kufikira m'matako, nawaleka achoke.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Hanuni anagwira anthu amene Davide anawatuma aja ndipo anawameta ndi kudula zovala zawo pakati mʼchiwuno mpaka matako kuonekera ndipo anawabweza kwawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Hanuni anatenga anyamata a Davide, nawameta, nadula malaya ao pakati kufikira m'matako, nawaleka acoke.