1 Chronicles 19:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Davide atamva zimenezo, adatuma Yowabu pamodzi ndi gulu lake lonse la ankhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene Davide anamva ichi anatuma Yowabu ndi gulu lonse la anthu amphamvu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide atamva zimenezi, anatumiza Yowabu ndi gulu lonse la ankhondo amphamvu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene Davide anamva ici anatuma Yoabu ndi gulu lonse la anthu amphamvu.