1 Chronicles 2:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yese adabereka Eliyabu mwana wake wachisamba, wachiŵiri Abinadabu, wachitatu Simea,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Yese anabala mwana wake wamwamuna woyamba Eliyabu, ndi Abinadabu wachiwiri, ndi Simea wachitatu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yese anabereka Eliabu mwana wake woyamba, wachiwiri Abinadabu, wachitatu Simea,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Jese anabala mwana wace wamwamuna woyamba Eliabu, ndi Abinadabu waciwiri, ndi Simeya wacitatu,