1 Chronicles 2:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kalebe mwana wa Hezironi anali nawo ana omubalira mkazi wake Azuba ndiponso Yerioti. Ana amene adabala mkaziyo naŵa: Yesere, Sobabu ndi Aridoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Kalebe mwana wa Hezironi anabala ana ndi Azuba mkazi wake, ndi Yerioti; ndipo ana ake ndiwo Yesere, ndi Sobabu, ndi Aridoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kalebe mwana wa Hezironi anabereka ana mwa Azuba mkazi wake (ndi mwa Yerioti). Ana a mkaziyo anali awa: Yeseri, Sobabu ndi Aridoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi Kalebi mwana wa Hezroni anabala ana ndi Azuba mkazi wace, ndi Yerioti; ndipo ana ace ndiwo Yeseri, ndi Sobabu, ndi Aridoni.