1 Chronicles 2:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Segubu adabereka Yairi amene anali ndi mizinda 23 m'dziko la Giliyadi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Segubu anabala Yairi, amene anali nayo midzi makumi awiri mphambu itatu m'dziko la Giliyadi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Segubu anabereka Yairi, amene anali ndi mizinda 23 ku Giliyadi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi Segubu anabala Yairi, amene anali nayo midzi makumi awiri mphambu itatu m'dziko la Gileadi.