1 Chronicles 2:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Yerameele, mwana wachisamba wa Hezironi, naŵa: Ramu mwana wachisamba, Buna, Oreni, Ozemu, ndi Ahiya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana a Yerameele mwana woyamba wa Hezironi ndiwo: woyamba Ramu, ndi Buna, ndi Oreni, ndi Ozemu, ndi Ahiya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Yerahimeeli, mwana woyamba wa Hezironi anali: Ramu, mwana wake woyamba, Buna, Oreni, Ozemu ndi Ahiya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana a Yerameli mwana woyamba wa Hezroni ndiwo: woyamba Ramu, ndi Buna, ndi Oreni, ndi Ozemu, ndi Ahiya.