1 Chronicles 2:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Ramu, mwana wachisamba wa Yerameele, anali Maazi, Yamini ndi Ekeri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana a Ramu mwana woyamba wa Yerameele ndiwo Maazi, ndi Yamini, ndi Ekeri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Ramu, mwana woyamba wa Yerahimeeli, anali awa: Maazi, Yamini ndi Ekeri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana a Ramu mwana woyamba wa Yerameli ndiwo Maazi, ndi Yamini, ndi Ekeri.