1 Chronicles 2:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Onamu anali Samai ndi Yada. Ana a Samai anali Nadabu ndi Abisuri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana a Onamu ndiwo Samai, ndi Yada; ndi ana a Samai: Nadabu, ndi Abisuri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Onamu anali awa: Shamai ndi Yada. Ana a Shamai anali awa: Nadabu ndi Abisuri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana a Onamu ndiwo Samai, ndi Yada; ndi ana a Samai: Nadabu, ndi Abisuri.