1 Chronicles 2:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Nadabu anali Seledi ndi Apaimu. Seledi adafa opanda ana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana a Nadabu: Seledi ndi Apaimu; koma Seledi anamwalira wopanda ana.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Nadabu anali awa: Seledi ndi Apaimu. Koma Seledi anamwalira wopanda ana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana a Nadabu: Seledi ndi Apaimu; koma Seledi anamwalira wopanda ana.