1 Chronicles 2:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wa Apaimu anali Isi. Mwana wa Isi anali Sesani. Mwana wa Sesani anali Alai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi mwana wa Apaimu: Isi. Ndi mwana wa Isi: Sesani. Ndi mwana wa Sesani: Alai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Apaimu anali awa: Isi, amene anabereka Sesani. Sesani anabereka Ahilai.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi mwana wa Apaimu: lsi. Ndi mwana wa lsi: Sesani. Ndi mwana wa Sesani: Alai.