1 Chronicles 2:32 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Yada mbale wa Samai anali Yetere ndi Yonatani. Yetere adafa opanda ana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana a Yada mbale wa Samai: Yetere, ndi Yonatani; namwalira Yetere wopanda ana.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Yada, mʼbale wa Samai, anali awa: Yereri ndi Yonatani. Koma Yeteri anamwalira wopanda ana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana a Yada mbale wa Samai: Yeteri, ndi Yonatani; namwalira: Yeteri wopanda ana.