1 Chronicles 2:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sesani analibe ana aamuna, anali ndi ana aakazi okhaokha. Koma anali ndi kapolo wake wa ku Ejipito, dzina lake Yara.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Sesani analibe ana amuna, koma ana akazi. Ndi Sesani anali naye mnyamata Mwejipito dzina lake ndiye Yara.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sesani sanabereke ana aamuna koma aakazi okhaokha. Iye anali ndi wantchito wa ku Igupto, dzina lake Yariha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Sesani analibe ana amuna, koma ana akazi. Ndi Sesani anali naye mnyamata M-aigupto dzina lace ndiye Yara.