1 Chronicles 2:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Sesani adakwatitsa mwana wake wamkazi kwa Yara kapolo wake uja. Ndipo mkaziyo adamubalira Attai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Sesani anampatsa Yara mnyamata wake mwana wake wamkazi akhale mkazi wake, ndipo anambalira Atai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sesani anapereka mwana wake wamkazi kwa Yariha wantchito wake kuti amukwatire ndipo anamuberekera Atayi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Sesani anampatsa Yara mnyamata wace mwana wace wamkazi akhale mkazi wace, ndipo anambalira Atai.