1 Chronicles 2:41 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Salumu adabereka Yekamiya, ndipo Yekamiya adabereka Elisama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Salumu anabala Yekamiya, ndi Yekamiya anabala Elisama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Salumu anali abambo a Yekamiya, Yekamiya anali abambo a Elisama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Salumu anabala Yekamiya, ndi Yekamiya anabala Elisama.