1 Chronicles 2:42 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Kalebe mbale wa Yerameele naŵa: Maresa, mwana wake wachisamba, bambo wake wa Zifi. Mwana wa Maresa anali Hebroni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana a Kalebe mbale wa Yerameele ndiwo Mesa mwana wake woyamba, ndiye atate wa Zifi; ndi ana a Maresa atate wa Hebroni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Kalebe mʼbale wa Yerahimeeli anali awa: Mesa mwana wachisamba, anali abambo a Zifi, ndipo mwana wake Maresa anali abambo a Hebroni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana a Kalebi mbale wa Yerameli ndiwo Mesa mwana wace woyamba, ndiye atate wa Zifi; ndi ana a Maresa atate wa Hebroni.