1 Chronicles 2:45 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wa Samai anali Maoni. Tsono Maoni adabereka Betezuri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi mwana wa Samai ndiye Maoni; ndipo Maoni ndiye atate wa Betezuri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wa Samai anali Maoni, ndipo Maoni anali abambo a Beti Zuri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi mwana wa Samai ndiye Maoni; ndipo Maoni ndiye atate wa Betizuri.