1 Chronicles 2:46 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nayenso Efa, mzikazi wa Kalebe, adamubalira Harani, Moza ndi Gazezi. Harani adabereka Gazezi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Efa mkazi wamng'ono wa Kalebe anabala Harani, ndi Moza, ndi Gazezi; ndi Harani anabala Gazezi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Efai, mzikazi wa Kalebe, anali amayi a Harani, Moza ndi Gazezi. Harani anali abambo a Gazezi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi Efa mkazi wamng'ono wa Kalebi anabala Harani, ndi Moza, ndi Gazezi; ndi Harani anabala Gazezi.