1 Chronicles 2:48 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maaka, mzikazi wa Kalebe, adamubalira Sebere ndi Tirihana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Maaka mkazi wamng'ono wa Kalebe anabala Sebere, ndi Tirihana.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Maaka mzikazi wa Kalebe anali mayi Seberi ndi Tirihana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Maka mkazi wamng'ono wa Kalebi anabala Seberi, ndi Tirana.