1 Chronicles 2:49 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkaziyo adabalanso Saafi, bambo wake wa Madimana, ndi Seva bambo wake wa Makibena ndiponso bambo wa Gibea. Mwana wamkazi wa Kalebe anali Akisa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iyeyu anabalanso Saafi atate wa Madimana, Seva atate wa Makibena, ndi atate wa Gibea; ndi mwana wamkazi wa Kalebe ndiye Akisa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anaberekanso Saafi abambo a Madimena ndi Seva abambo a Makibena ndi Gibeya. Mwana wamkazi wa Kalebe anali Akisa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iyeyu anabalanso Safa atate wa Madimana, Seva atate wa Makibena, ndi atate wa Gibeya; ndi mwana wamkazi wa Kalebi ndiye Akisa.