1 Chronicles 2:50 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ameneŵa ndiwo amene anali zidzukulu za Kalebe. Ana a Huri, mwana wachisamba wa Efurata, naŵa: Sobala amene adabereka Kiriyati-Yearimu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Kalebe ndi awa: mwana wa Huri, mwana woyamba wa Efurata, Sobala atate wa Kiriyati-Yearimu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Izi zinali zidzukulu za Kalebe. Ana a Huri mwana wachisamba wa Efurata anali awa: Sobala abambo a Kiriati Yearimu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Kalebi ndi awa: mwana wa Huri, mwana woyamba wa Efrata, Sobali atate wa Kiriate Yearimu.