1 Chronicles 2:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Karimi naŵa: Akara amene adaavuta Aisraele. Iyeyo adaaba zinthu zoyenera kuziwononga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana a Karimi: Akara wovuta Israeleyo, amene analakwira choperekedwa chiperekerecho.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wa Karimi anali Akani, amene anabweretsa mavuto pakati pa Israeli pamene anatenga zinthu zoyenera kuwonongedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana a Karmi: Akari wobvuta Israyeliyo, amene analakwira coperekedwa ciperekereco.