1 Chronicles 20:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku lina pamene adanyoza Aisraele, Yonatani, mwana wa Simea, mbale wake wa Davide, adamupha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo potonza Israele iyeyu Yonatani mwana wa Simea mbale wake wa Davide anamkantha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene iye ankanyoza Aisraeli, Yonatani mwana wa Simea, mʼbale wake wa Davide anamupha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo potonza Israyeli iyeyu Yonatani mwana wa Simeya mbale wace wa Davide anamkantha.