1 Chronicles 20:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthuwo anali zidzukulu za Arefaimu a ku Gati, ndipo adaphedwa ndi Davide ndi ankhondo ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Awa anabadwa mwa chimphonacho ku Gati, koma anagwa ndi dzanja la Davide ndi la anyamata ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu amenewa anali zidzukulu za Rafa ku Gati, ndipo anaphedwa ndi Davide ndi ankhondo ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Awa anabadwa mwa cimphonaco ku Gati, koma anagwa ndi dzanja la Davide ndi la anyamata ace.