1 Chronicles 21:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Pita ukamuuze Davide kuti, Ine Chauta ndikunena kuti, ‘Ndikuika pamaso pako zinthu zitatu zoti ndikuchite. Tsono usankhepo chimodzi ndipo ndidzakuchita.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kanene kwa Davide kuti, Atero Yehova, Ndikuikira zitatu; dzisankhireko chimodzi ndikuchitire ichi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Pita ukamuwuze Davide kuti, ‘Yehova akuti, Ine ndikukupatsa zinthu zitatu izi. Usankhepo chimodzi pa zimenezi choti ndikuchitire.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kanene kwa Davide kuti, Atero Yehova, Ndikuikira zitatu; dzisankhireko cimodzi ndikucitire ici.