1 Chronicles 21:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo mngelo wa Chauta adalamula Gadi kuti, “Kauze Davide kuti akamangire Chauta guwa pa malo opunthira tirigu a Orinani Myebusi uja.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo mthenga wa Yehova anauza Gadi kuti anene ndi Davide, akwere Davideyo kuutsira Yehova guwa la nsembe pa dwale la Orinani Myebusi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo mngelo wa Yehova analamula Gadi kuti awuze Davide kuti akamange guwa lansembe la Yehova pamalo opunthira tirigu a Arauna Myebusi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo mthenga wa Yehova anauza Gadi kuti anene ndi Davide, akwere Davideyo kuutsira Yehova guwa la nsembe pa dwale la Orinani Myebusi,