1 Chronicles 21:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho Davide adauza Yowabu mtsogoleri wa ankhondo kuti, “Pita, ukaŵerenge Aisraele kuyambira ku Beereseba mpaka ku Dani, ndipo udzandiwuze, kuti ndidziŵe chiŵerengero chao.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Davide anati kwa Yowabu ndi kwa akulu a anthu, Kawerengeni Israele kuyambira ku Beereseba kufikira ku Dani; nimundibwezere mau, kuti ndidziwe chiwerengo chao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Davide anati kwa Yowabu pamodzi ndi atsogoleri a ankhondo, “Pitani mukawerenge Aisraeli kuyambira ku Beeriseba mpaka ku Dani. Ndipo mudzandiwuze kuti ndidziwe chiwerengero chawo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Davide anati kwa Yoabu ndi kwa akuru a anthu, Kawerengeni Israyeli kuyambira ku Beereseba kufikira ku Dani; nimundibwezere mau, kuti ndidziwe ciwerengo cao.