1 Chronicles 21:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'menemo nkuti Orinani akupuntha tirigu. Atacheuka adaona mngeloyo, koma ana ake aamuna anai amene anali naye, adaabisala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pocheuka Orinani anaona wamthengayo; ndi ana ake amuna anai anali naye anabisala. Koma Orinani analikupuntha tirigu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Arauna ankapuntha tirigu, anatembenuka ndipo anaona mngelo ndipo ana ake anayi aamuna amene anali naye anabisala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Poceuka Orinani anaona wamthengayo; ndi ana ace amuna anai anali naye anabisala. Koma Orinani analikupuntha tirigu.