1 Chronicles 21:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Davide sadathe kupitako kukapempha nzeru kwa Mulungu, poti ankachita mantha ndi lupanga la mngelo wa Chauta uja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Davide sanathe kumuka kukhomo kwake kufunsira kwa Mulungu, pakuti anaopa lupanga la mthenga wa Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Davide sanathe kupita kumeneko kuti akapemphere pamaso pa Yehova, chifukwa amaopa lupanga la mngelo wa Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kama Davide sanathe kumuka kukhomo kwace kufunsira kwa Mulungu, pakuti anaopa lupanga la mthenga wa Yehova.