1 Chronicles 22:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iyeyo ndiye adzandimangire nyumba. Adzakhala mwana wanga, Ine ndidzakhala bambo wake, ndipo ndidzakhazikitsa mpando wake waufumu m'dziko la Israele mpaka muyaya.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
iyeyu adzamangira dzina langa nyumba; iye adzakhala mwana wanga, ndi Ine ndidzakhala Atate wake; ndipo ndidzakhazikitsa mpando wachifumu wa ufumu wake pa Israele, kosalekeza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye ndiye adzandimangire nyumba. Adzakhala mwana wanga ndipo Ine ndidzakhala abambo ake. Ndipo ndidzakhazikitsa mpando wake waufumu mʼdziko la Israeli mpaka muyaya.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
iyeyu adzamangira dzina langa nyumba; iye adzakhala mwana wanga, ndi Ine ndidzakhala Atate wace; ndipo ndidzakhazikitsa mpando wacifumu wa ufumu wace pa Israyeli kosalekeza.