1 Chronicles 22:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Davide adaonjeza kuti, “Tsono mwana wanga, Chauta Mulungu wako akhale nawe, kuti udzathe kummangira nyumba monga m'mene wanenera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsono, mwana wanga, Yehova akhale nawe; nulemerere, numange nyumba ya Yehova Mulungu wako monga ananena za iwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsopano mwana wanga, Yehova akhale nawe ndipo upambane ndi kumanga Nyumba ya Yehova Mulungu wako, monga momwe Iye ananenera kuti udzatero.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsono, mwana wanga, Yehova akhale nawe; nulemerere, numange nyumba ya Yehova Mulungu wako monga ananena za iwe.