1 Chronicles 22:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe Chauta akuninkhe nzeru ndi luntha, kuti akadzakupatsa ulamuliro woyang'anira Israele, udzasunge malamulo a Chauta Mulungu wako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chokhachi, Yehova akupatse nzeru ndi luntha, nakulangize za Israele, kuti usunge chilamulo cha Yehova Mulungu wako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova akupatse nzeru ndi kumvetsetsa pamene Iye adzakuyika kukhala wolamulira Israeli, kuti udzasunge malamulo a Yehova Mulungu wako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cokhaci, Yehova akupatse nzeru ndi luntha, nakulangize za Israyeli, kuti usunge cilamulo ca Yehova Mulungu wako,